“ Prophet Habakuku sindikuwa User, anachita kundipeza okha pano ndife Duo “
Zacks Chihana wafokoza za m’mene adakumanilana ndi Prophet Habakuku kuti mpaka aziyimba ngati Duo.
“ Ine Zack’s chihana, ninabadwika mu boma la Rumphi koma kukulila kwanga ndakulila mu Zambia, ndikomwe ninayamba zoimba ndiye ndita bwela kuno ku malawi ndinali ndi show itatha after 3 days ninalindila fone kuchoka Kwa Prophet Habakuku akuti tiimbe nyimbo tipange collaboration from there ninavomela ndipo anandiitana kupita ku chitipa mpaka lero ndife Duo.
Nde ena akamati ndikuwa user kapena kuwadyela aziziwa kuti anachita kundipeza okha” – Watero Zacks
Leave a Reply