Yalakwa Ku Australia. Mayi wina anapita ku chipatala cha Monash IVF kuti athe kutenga mimba kudzera mu njira ya sayansi. Imene amamuyika embryo mu mimba.
Zinthu zinali bwino mpaka poti anatenga mimba.
Koma mbola ! Embryo imene adamuyika mu mimba mayiyu si ya mwana wake!
Ena akuti chipatala chinaphatikiza ma embryo molakwika – ndiye mwana uja anali wa banja lina osati la mkazi uja.
Nthawi itapita, mwana anabadwa ali bwino, koma mayi uja powona ali “Nooooo! Uyu si mwana wanga”. Mzungu ubeleka bwanji Chinese ?
Mpaka chipatala chitayeza DNA chapezadi kuti mwana anabadwitsa mayiyo si wawodi.
CEO wa chipatalacho wayesesa kupepesa kuti izi sizizachitikanso ndipo akaka nkoyamba koma Mayiyu wangokhala okhumudwa.
Couple ina imene Embryo idali yawo awafikila kuwawuza zoti mayi wina wabadwitsa mwana wawo koma nawo angokhala otutumuka
MAYI ALILA ATATENGA MIMBA YOTI SIYAKE
Yalakwa Ku Australia. Mayi wina anapita ku chipatala cha Monash IVF kuti athe kutenga mimba kudzera mu njira ya sayansi. Imene amamuyika embryo mu mimba. Zinthu zinali bwino mpaka ...
By editor·April 8, 2026·2 min read
58


More in artificial intelligence
artificial intelligenceeditor
Dr. Dre embraces AI as a new tool for music creation
American hip-hop legend Dr. Dre has revealed that he is using artificial intelligence (AI) in the process of making new…
10 1
artificial intelligenceeditor
AI Designs New Viruses in Laboratory
US researchers have demonstrated that artificial intelligence can be used to design entirely new viruses capable of func…
77 1
artificial intelligenceeditor
Diddy’s Prison Release Date Moved to February 2028, Latest Bureau of Prisons Update Shows
The projected release date for American music mogul Sean Combs has been updated again, with federal records now showing…
253 0


