Bungwe la Lagos State Internal Revenue Service (LIRS) lasindikiza za kutsekedwa kwa sitolo ya Shoprite yomwe ili ku Ikeja City Mall, litati kampaniyo yalephera kutsatira malamulo ake okhudza kulipira misonkho. Malinga ndi LIRS, kutsekedwa kumeneku ndi gawo la kampeni yolimbikitsa kuti mabizinesi onse omwe amagwira ntchito mu mzinda wa Lagos azilipira misonkho moyenera.
Kutsekedwaku kwachitika lero ndipo kwadabwitsa ogula komanso okhalamo omwe nthawi zambiri amapita ku malo ogulitsirawo. A LIRS ati akhala atumiza mawuthenga owachenjeza kangapo kwa oyang’anira sitolo ya Shoprite koma sanatsatire zomwe amalamulidwa.
Pomwe LIRS lati zomwe apangazi ndi zovomerezeka komanso yachizolowezi pa ntchito zawo zowona kuti ndondomeko ya mmisonkho ikutsatilidwa. Padakali pano anthu ambiri akudikirira kuona zomwe Shoprite iyankhe pa zomwe ikuwaganizirazi. Sitoloyo ikhala yotsekedwa mpaka kampaniyo itakhazikitsa malamulo onse ndikutsimikizira kutsatira kwake kwa misonkho.
LIRS Yatseka Sitolo ya Shoprite ku Ikeja City Mall Chifukwa cha Misonkho
Bungwe la Lagos State Internal Revenue Service (LIRS) lasindikiza za kutsekedwa kwa sitolo ya Shoprite yomwe ili ku Ikeja City Mall, litati kampaniyo yalephera kutsatira malamulo a...
By editor·April 8, 2026·2 min read
304

More in business
businesseditor
BINANCE FACES SUSPECTED $5.8 BILLION CRYPTO HACK
The world’s largest cryptocurrency exchange, Binance, is reportedly investigating a massive security breach involving cr…
23 0
businesseditor
IMM recognises Bright Chiligo for contribution to marketers’ conference
Digital entrepreneur and Mikozi Founder Bright Chiligo has been recognised by the Institute of Marketing in Malawi (IMM)…
5403 1
businesseditor
PayPal has launched its digital dollar, PayPal USD (PYUSD), in Malawi and 26 other African countries.
In a statement, the company said the service allows users to buy, hold, send and receive the digital currency through Pa…
1669 0


