Save 20% off! Join our newsletter and get 20% off right away!

Bambo wina ku America wapezeka olakwa ndipo alandira chilango chofanana ndikupha munthu pa mulandu umene mwana wake anakapanga zaupandu ndikupha ana asukulu anzake pogwilitsa ntchito mfuti umene bambowa anamugulira ngati mphatso ya khirisimisi