Save 20% off! Join our newsletter and get 20% off right away!

Ku Nigeria zafika poti Galu akumamushawuwa osati masewera. Dog meat ikudyedwa kuposa dziko lililonse ku Africa komanso Ali pa number 3 mu dziko lonse. Kaya Spanner Malawi uja sanakadyeko ka dog meat peppe soup kumeneko😂