Oyimba, Nepman wati oyimba amzake omwe ndi amene akhala akumukhomelela kulinka ndi oyimba akunja.
Iyeyu wati ;-
Mu industry ya music ku Malawi inachuluka nsanje maka kwa oyimba tokhatokhafe.
Ma artist ena anzanga ochokera ku Malawi atabwera kuno ku Zambia akhala akupemphedwa nambala yanga koma zachisoni anthuwo amayankha kuti nambala yanga alibe pomwe alinayo.
Nde anthu omwewo akudabwa mmene ndikupelekera ma nambala a oyimba anzanga. Ndinkona oyimba ena akuluakulu amakhomelera ma upcoming artist kuopa kuti awaposa.
Mukapitiliza makhalidwe a nsanje munatipeza mu industry ndipo muzatisiya “
Leave a Reply