“ Prophet Habakuku sindikuwa User, anachita kundipeza okha pano ndife Duo “
Zacks Chihana wafokoza za m’mene adakumanilana ndi Prophet Habakuku kuti mpaka aziyimba ngati Duo.
“ Ine Zack's chihana, ninabadwika mu boma la Rumphi koma kukulila kwanga ndakulila mu Zambia, ndikomwe ninayamba zoimba ndiye ndita bwela kuno ku malawi ndinali ndi show itatha after 3 days ninalindila fone kuchoka Kwa Prophet Habakuku akuti tiimbe nyimbo tipange collaboration from there ninavomela ndipo anandiitana kupita ku chitipa mpaka lero ndife Duo.
Nde ena akamati ndikuwa user kapena kuwadyela aziziwa kuti anachita kundipeza okha” - Watero Zacks
Prophet Habakuku sindikuwa User, anachita kundipeza okha
“ Prophet Habakuku sindikuwa User, anachita kundipeza okha pano ndife Duo “ Zacks Chihana wafokoza za m’mene adakumanilana ndi Prophet Habakuku kuti mpaka aziyimba ngati Duo. “ Ine...
By editor·April 8, 2026·2 min read
59


More in entertainment
entertainmenteditor
Tiwa Savage promises collaboration with Temwah
Nigerian music superstar Tiwa Savage has pledged to collaborate with Malawian singer Temwah on a song and music video, a…
3605 1
entertainmenteditor
Nicolas Cage Claims He May Remember Being in His Mother’s Womb
Hollywood actor Nicolas Cage once made a bizarre claim about what he believes could be his earliest memory — saying he s…
397 1
entertainmenteditor
Beyoncé Becomes Richest Black Female Music Artist, Surpasses US$1 Billion Net Worth
Beyoncé has cemented her place as the world's richest Black female music artist, with her net worth surpassing the US$1…
269 1


