Ma celebrity ku Malawi ayamba kunyanyala zogula ma condom in public places chifukwa cha manyazi komanso mantha potengera kuti tili mu nthawi yoti anthu akumajambula ndikuyika pa social media zilizonse makamaka zikakhala zokhuza anthu odziwika.
Izi zadziwika pamene celeb wina wamu Lilongwe wodziwika ndikuyimba nyimbo zachikondi wanena poyera kuti amakanika kugula ma condoms powopa kuti anthu amujambula ndikumuika pamasamba a mchezo apa social media.
“Man, ine zogula ma condoms in public places ndizituluka. Imagine if someone takes a photo and it goes viral on social media? People would start speculating especially since I’m married. I’d be the headline before I even got home”, he said.
As funny as it sounds this is happening and it’s a clear reminder that even stars we put on pedestals feel everyday embarrassment. In this era of cameras, smartphones, and social media something as simple as buying condoms is a public spectacle to celebrities.










Leave a Reply